[Lyrics] Wikise – Belu

INTRO
Owuooooh
Owuooooooooooh
Owuowoooooo (Emama namalenga eeh)
Owuooooh
Owuooooooooooh
Owuowoooooo (ambuye namalenga baba)
VERSE 1
Satana walisochelesa dziko (kuno)
Zinthu zoipa anthu ayesa zabwino (nyasi)
Koma ambuye zili kuno
Anthu akonda ndalama
Kuposa moyo wa munthu
Akakhuta migayiwa
Mayambisa timabungwe ati orphanage chani chani
Akalandila fund
Kumagula tima mira
Nkumati shanila (nkumatilanda akazi)
Can you imagine ambuye
Azimayi oyima kuseli kwa crossroads
mpaka kukhala ndi association
Kumapanga mademo
Enough is enough basi
CHORUS
Ambuye Imbani Belu uu
Nthawiiiiii
Dziko kuno laonongeka aaah (dziko lanunkha enough is enough basi?
Yehova Imbani Belu uu
Nthawi iii
Dziko kuno laonongeka aaah (dziko lanunkha)
VERSE 2
Atumiki anu anakutulukani
Amangolalikira za ndalama
Dzina lanu pano ndi mpamba
Imbani lipengalo lilire
(Trumpet)
Akumatiuza pelekani molowa manja
Ulemelero wathu uli Kumwamba
Iwo namagula magalimoto
Ife namayenda napatapata
Musatemero Angelo
Ingoyimbani belu
Anthu chilungamo pansi
Angelo anu azawadyesa Banzi.
BACK TO CHORUS
Ambuye Imbani Belu uu
Nthawiiiiii
Dziko kuno laonongeka aaah (dziko lanunkha enough is enough basi?
Yehova Imbani Belu uu
Nthawi iii
Dziko kuno laonongeka aaah (dziko lanunkha)
OUTRO
Achuluka ndi adyela
Opondeleza Imbani belu baba
THE END