Entertainment NewsUncategorized
Achule…mu rap game muli achule

Achule…mu rap game muli achu
Ma guys oti hit song anatulutsa 10 years ago koma kumangoipopa daily.. Achule
- Ma guys oti akafuna kutulutsa nyimbo, amakajambulitsa atavula nkukhala pa mtondo wa toilet.. Achule
- Ma guys oti ukawauza kuti nyimbo yawo siyabwino basi kumakuopsyeza kuti akupatsa makofi..achule
- Ma guys oti akafuna kumenya tracks ndi female emcee basitu amafuna amukwele. Achule
- Maguys oti ndi ma veteran koma akafuna beat or akafuna video kwa ma producers basi ati afuna za ulere. Ati exposure. Achule
- Ma guys oti akayambana ndi azibutsa oti anawachosa mu umphawi basi kumapanga zopepela kuti awoneke abwino iwowo..Achule
- Ma event organizers osapeleka dollar mwachangu…achule Achule ndi ambiri!