International News
Top 100 bars from Krazie G

10- ati ndikutukwana when i say : they cant
9- Akazi aku Malawi akumazimva aku spain chifukwa akandiona amandi Puta
8- Mphaka wakwaneba akabwera kwanu ndipamene iweyo umaona Pussy
7- Ndine mfana otentha, ndimatafuna makala
6- Got a bad relationship with the radio; it plays me
5- Fanz ndimaibanda ngati ganja ndikupotayi
4- Ndikudya paper koma akumva kuwawa ndi wina
3- Sine wa ma looks ndine nkhwanga, koma akazi ndi nkhuni chifukwa ndi mawawaza
2- akazi amene ndinkawafuna pano sindimawafuna/ ankandiuza kuti ali ndi mamumana pano akuti ndine mwamwunA91- Nigga am the shit ask sewage tanks
1- akazi kundikakamila ngati K pa Kenya/ akandifunsila machosa K yo ndikuti EnyaKrazie WeekTo be continued~phomdiga