Entertainment News
BlakJak dates Made See

Mphangala Ku nkhani za mayimbidwe a dancehall Black Jak wati amuyitanisa Made See pa wailesi ya kanema kuti a Malawi amve mbali yake bwinobwino.Izi zaza pamene a Malawi ambiri anamuthila mphepo mwanayi chifukwa cha mtima osayamika.
BlakJak wati tisathamangile kumuweluza koma timpase mpata afotokoze bwino bwino zimene zasokoneza ubale wawo ndi Dr Namadingo Tili likiliki kudikira interview imeneyi koma akamva mbali ya Made See apangenso machawi omwewo nkumuyitana Doctor timve mbali yake.
Blakjakmw #madesee #namartists