Entertainment News
Young Kay aka Hyphen uja has put so many people on

In his first albums anamupasa mpata ‘ Maskal’. Maskal anamenya ma hook anyimbo zambirimbiri monga Manvelamvela ndi Photobook. Nthawi imeneyo a Maskal sanali otchuka kwambiri. Anamupasa platform and he blew up after that.
Anamupasanso platform Oenismus uja ali Armstrong mu Pauchidolo the Mixtape. Nthawi imeneyo a Armstrong anali asanafikepo. Anali akuyimba za zimwale. Koma mu Pauchidolo mixtape anawapasa mpata oti aziyimbako nyimbo zamakono komanso za chizungu. Nyimbo ngati Pauchidolo, Do or Die and ndili pompo.
Young Kay apapa pokha ofunika kumpasa ulemu