Tremour – Mpanipani song Lyric

Mhu”’
Mvera again//
Tamvera again//
Mvera again//
Tamverani again
(One Genious Turn)
Kodi uli sure
Mphamvu zako zonse ukasonkheza
Tandiuza uli serious
Kukhala potelopo msonzi nkumakhetsa
Walimba mtima wasting energy in stressing
Spending hours on regretting
Anzako ali mkaliki liki kugogoda ma gate
Achakwera ali story sanayambe chonchi peza nthawi ufufuze
Simama ali ndi story enawa nduwaziwa bwino anali amabuku ndi news paper
Ulimba mtima wasting energy in stressing
Spending hours on regretting
Anzako ali mkali liki kugogoda ma gate
Usaziyike pa pressure
Success yawo isakupatse mpanipani
Only you know yourself better
There is one version of you ulipo wekha
Ngwa mwachitidwe ake
Ngwa dongosolo lake
Ngwa nthawi yake
Ngwa masovedwe ake Yehovah
Ali nayo yake yake
Ali nayo yake yake
Ali nayo yake yake
Yako yako file special kumwambako iliko
Ya mzako osachita nayo chidikho dikho
Fatsa akukukonzera mapiko
Udzakhala star pamwamba padziko
Sanayambe chonchi Gaba
Ndipo zoti adzakhala shasha
Ingakhale amayi ake sankadziwa ata
Achakwera ali story sanayambe chonchi peza nthawi ufufuze
Simama ali ndi story enawa nduwaziwa bwino anali amabuku ndi news paper
Usaziyike pa pressure
Success yawo isakupatse mpanipani
Only you know yourself better
There is one version of you ulipo wekha
Usaziyike pa pressure
Success yawo isakupatse mpanipani
Only you know yourself better
There is one version of you ulipo wekha
Ngwa nthawi yache
Ngwa machitidwe ache
Ngwa masovedwe ache
Ali ndi Mphamvu yake Yehovah
(Yako yako file special kumwambako iliko
Ya mzako osachita nayo chidikho dikho
Fatsa akukukonzera mapiko
Udzakhala star)
Usaziyika pa pressure
Success yawo isakupatse mpanipani
Only you know yourself better
There is one version of you ulipo wekha
Ngwa mwachitidwe ake
Ngwa dongosolo lake
Ngwa nthawi yake
Ngwa masovedwe ake Yehovah
WRITTEN, COMPOSED & COMPILED BY TREMOUR