Zimveke Bwa? Lyrics

Zimveke Bwa? Lyrics
uuh muti zimveke bwa? uh huh
H-Y-P-H…
Hyphen verse 1
ah ah ukukaika
chiphona chogona, chi master chomaliza
huh, chi mfana cholaiva, chosaimva
olo Ichocho ku saizaaa
osaphweketsa we rarely socialize
positive vibes we polarize
musunge chithumba if ever you call on us
bruh every building we been in we colonize
bar after bar after bar chiku charger
kuthuzula, kuphuzula ngati Mchacha
look who you are, never been part of the culture
mafana okula mosemphana ndi makhatcha
chorus
Inu mmati zimveke bwa?
mwaputa olakwika mupweteka
osamangotamika kuphweketsa
sitiyimva, lero mupepesa, mupepesa
Hyphen verse 2
nde, nde nkachekela, tchekela
khonfi yangolomela kutelela
kamunthu umakakondako, tsekela
kujama ya ife uzaona polekela
take shots popanda kuphelela
take notes mafana akuchepela
zikawawa tisanza, sitimezela
tikakunyala tiku halla sitizembelaaa
mafana a tchubu otilemela
play the part sitidanda zotisemela
ka utsi kazomelela, ka mwano kutiyenela
nthano zanuzo mukuti zimveke bwa?
Achina Gattah Verse 3
yoh, show ya usiku ndi ma G
koma zomwe zachitika iwe iiih
kuchezela kuyatsa moto ngati ovuni
ine ndi smoke aise ndi fake mchumuni
ndinasowa pakati ndinavaya,
ndimakagwila bele kwa yaya
mwina sumadziwa ndinazama man
nkona ndiku hitta kuposa nyimbo za ma man
koma, mafana adhiwawa, kupandipanga nkhanza man
dzulo ndakumana ndi Mandela pa Mwanza man
akuti a Gattah muli sick mukusanza man
ndati eeh ndimatha kwambiri ndine sanza man
ngati Ice Prince, udolo nnamaliza man
streets is safe I run
iwe, ndani akupanga makani
Inu, ckuf you all I’m done